Pakhomo

Language: Chichewa
Khristu Mu Nyimbo

Pakhomo

[1]
Mpulumutsi Pakhomopo! Agogoda mofatsa tu,
Walindira, alindabe, Musamcitire cipongwe.

2. Akulangiza ugule Golide yo ndi Cobvala;
Dzoza maso, muonetu, Ucotse zonyasa zako.

[3]
Mvera mau a umboni Ati usanke wacedwa;
Uli wonyoza, wofunda! Khala cangu usanduke.

[4]
Ncito yayandika kutha, Kudandaulira kutha;
Wonynsa anyansebe tu, Woyera akhalebe conco.

[5]
Lonyowa tsitsi ndi mame, Cifukwa akukondadi,
Dzuka! Tsegula citseko; Muuze asacedwenso.

[6]
Alowe wokondedwayo; Upume pamaso pace.
Mwa ciyanjano cokoma Ndzadye naye, Iye nane.


Most Liked Songs
song image
1. Thanthwe Long’ambika

Khristu Mu Nyimbo

song image
2. Mukhale Ndine

Khristu Mu Nyimbo

song image
3. Kodi Yesu Asamala

Khristu Mu Nyimbo

song image
4. Bwinoli Tipita

Khristu Mu Nyimbo

song image
5. Sing’anga Mkuru Ndiye Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
6. Pokhala Mtendere

Khristu Mu Nyimbo

song image
7. Inenso

Khristu Mu Nyimbo

song image
8. Kuli Bwanji Kwathu

Khristu Mu Nyimbo

song image
9. Akulowa M’zipata

Khristu Mu Nyimbo

song image
10. Akristu Limbikani!

Khristu Mu Nyimbo

song image
11. Pakwitana Mbuye Wanga

Khristu Mu Nyimbo

song image
12. Inetu Ndifunadi

Khristu Mu Nyimbo

song image
13. Akristu Tiyeni

Khristu Mu Nyimbo

song image
14. Ulemu Kwa Mulungu

Khristu Mu Nyimbo

song image
15. Akan’stogoza Ndinkako

Khristu Mu Nyimbo

song image
16. A M’dziko Akondweratu

Khristu Mu Nyimbo

song image
17. Ndidze Pafupipa

Khristu Mu Nyimbo

song image
18. Tiribe Mzinda M’dzikoli

Khristu Mu Nyimbo

song image
19. Ambuye, Ndiri Kudza

Khristu Mu Nyimbo

song image
20. Pakakhala Cikondi

Khristu Mu Nyimbo

song image
21. Ambuyanga Yesu, Ndikonda Inu

Khristu Mu Nyimbo

song image
22. Dziko Ai, Koma Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
23. Bwenzi Lathu Ndiye Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
24. Muli Dzuwa M’phiri Muja

Khristu Mu Nyimbo

song image
25. Linda Usadandaule

Khristu Mu Nyimbo

song image
26. Iripo Nyimbo Ndikonda

Khristu Mu Nyimbo

song image
27. Poyemnda Ndi Mbuye

Khristu Mu Nyimbo

song image
28. Ndidzamdziwa Mombolo Wanga

Khristu Mu Nyimbo

song image
29. Mzimu Ndi Mtsogoziyo

Khristu Mu Nyimbo

song image
30. Analonjeza Ambuye Wathu

Khristu Mu Nyimbo