Akristu Tiyeni

Language: Chichewa
Khristu Mu Nyimbo

Akristu Tiyeni

[1]
Akristu tiyeni! Nkhondo tigwira,
Yesu Mbuye wathu, Atitsogoza,
Ona mbuye yekha, Atithanziza;
Ndi mbendera yace, Tiyitsatira.

CHORUS
Akristu tiyeni! Nkhondo tigwire,
Yesu Mbuye wathu, Atitsogoza.

[2]
Nkhondo ya Satana, Msanga ithawa,
Akristu tiyeni, Tidzapambana;
Mphamvu zace zitha, Yesu titama;
Timbani anzathu Nyimbo tikweza.

[3]
Gulu larikulu, Adza Akristu;
Titsatana namwo, Ana a Mlungu;
Sitipatukana, Tonse tikhala,
ndi mtima umodzi, Timakondana.

[4]
Zonse za pa dziko, Zidzatheratu;
Koma mpingo wace, Ukhalitsabe;
Mphamvu ya Satana, idzalefuka;
Yesu nalonjeza ndidzalimbitsa.

[5]
Idzani Akristu, Kutithandiza,
Nyimbo za Mulungu, tidzayimbitsa;
Kristu ayenera, Ndiye Mfumuyo,
Tidzalemekeza, Nthawi zonsezo.


Most Liked Songs
song image
1. Thanthwe Long’ambika

Khristu Mu Nyimbo

song image
2. Kodi Yesu Asamala

Khristu Mu Nyimbo

song image
3. Mukhale Ndine

Khristu Mu Nyimbo

song image
4. Bwinoli Tipita

Khristu Mu Nyimbo

song image
5. Sing’anga Mkuru Ndiye Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
6. Pokhala Mtendere

Khristu Mu Nyimbo

song image
7. Inenso

Khristu Mu Nyimbo

song image
8. A M’dziko Akondweratu

Khristu Mu Nyimbo

song image
9. Kuli Bwanji Kwathu

Khristu Mu Nyimbo

song image
10. Akristu Limbikani!

Khristu Mu Nyimbo

song image
11. Akulowa M’zipata

Khristu Mu Nyimbo

song image
12. Pakwitana Mbuye Wanga

Khristu Mu Nyimbo

song image
13. Inetu Ndifunadi

Khristu Mu Nyimbo

song image
14. Iripo Nyimbo Ndikonda

Khristu Mu Nyimbo

song image
15. Muli Dzuwa M’phiri Muja

Khristu Mu Nyimbo

song image
16. Ulemu Kwa Mulungu

Khristu Mu Nyimbo

song image
17. Akristu Tiyeni

Khristu Mu Nyimbo

song image
18. Ndidze Pafupipa

Khristu Mu Nyimbo

song image
19. Ambuye, Ndiri Kudza

Khristu Mu Nyimbo

song image
20. Maso Ndi Maso

Khristu Mu Nyimbo

song image
21. Akan’stogoza Ndinkako

Khristu Mu Nyimbo

song image
22. Tiribe Mzinda M’dzikoli

Khristu Mu Nyimbo

song image
23. Poyemnda Ndi Mbuye

Khristu Mu Nyimbo

song image
24. Dziko Ai, Koma Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
25. Ambuyanga Yesu, Ndikonda Inu

Khristu Mu Nyimbo

song image
26. Bwenzi Lathu Ndiye Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
27. Yesu Tsogolereni

Khristu Mu Nyimbo

song image
28. Pakakhala Cikondi

Khristu Mu Nyimbo

song image
29. Linda Usadandaule

Khristu Mu Nyimbo

song image
30. Tifuna Mzimu wanuyo

Khristu Mu Nyimbo