Poyemnda Ndi Mbuye

[1]
Poyenda ndi Mbuye, mkuwala kwaceko, Aunikira m’njira mwathu;
Pakugwaira ntchito amakhala nafe, Ndi onse amene amvera.

CHORUS
Khulupira, palibenso njira, Yakukondwa mwa Yesu,
Komatu kumvera.

[2]
Mthunzi sungagwetu, pena mtambo mmwamba, Komatu azipirikitsa;
Nkhawa ndi cisoni zidzacoka ngati, Tikhulupira ndi kumvera.

[3]
Cifukwa ca ntchito ndi zisoni zathu, Mpaka titadziperekatu;
Cifukwa cifundo ndi cimwemwe cace, Amapatsa anthu omvera.

[4]
Pompo mciyanjano tidzakhala naye, Kapena kuyenda ndi Iye;
Ndipo tidzacita cifuniro cace, Tidzakhala omvera ndithu.


Most Liked Songs
song image
1. Thanthwe Long’ambika

Khristu Mu Nyimbo

song image
2. Kodi Yesu Asamala

Khristu Mu Nyimbo

song image
3. Mukhale Ndine

Khristu Mu Nyimbo

song image
4. Bwinoli Tipita

Khristu Mu Nyimbo

song image
5. Sing’anga Mkuru Ndiye Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
6. Pokhala Mtendere

Khristu Mu Nyimbo

song image
7. Inenso

Khristu Mu Nyimbo

song image
8. Kuli Bwanji Kwathu

Khristu Mu Nyimbo

song image
9. Akulowa M’zipata

Khristu Mu Nyimbo

song image
10. Akristu Limbikani!

Khristu Mu Nyimbo

song image
11. Ulemu Kwa Mulungu

Khristu Mu Nyimbo

song image
12. Inetu Ndifunadi

Khristu Mu Nyimbo

song image
13. Akristu Tiyeni

Khristu Mu Nyimbo

song image
14. Ambuyanga Yesu, Ndikonda Inu

Khristu Mu Nyimbo

song image
15. A M’dziko Akondweratu

Khristu Mu Nyimbo

song image
16. Dziko Ai, Koma Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
17. Akan’stogoza Ndinkako

Khristu Mu Nyimbo

song image
18. Pakakhala Cikondi

Khristu Mu Nyimbo

song image
19. Tiribe Mzinda M’dzikoli

Khristu Mu Nyimbo

song image
20. Pakwitana Mbuye Wanga

Khristu Mu Nyimbo

song image
21. Bwenzi Lathu Ndiye Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
22. Ambuye, Ndiri Kudza

Khristu Mu Nyimbo

song image
23. Ndidze Pafupipa

Khristu Mu Nyimbo

song image
24. Iripo Nyimbo Ndikonda

Khristu Mu Nyimbo

song image
25. Linda Usadandaule

Khristu Mu Nyimbo

song image
26. Muli Dzuwa M’phiri Muja

Khristu Mu Nyimbo

song image
27. Poyemnda Ndi Mbuye

Khristu Mu Nyimbo

song image
28. Ndidzamdziwa Mombolo Wanga

Khristu Mu Nyimbo

song image
29. Analonjeza Ambuye Wathu

Khristu Mu Nyimbo

song image
30. Mzimu Ndi Mtsogoziyo

Khristu Mu Nyimbo