Kodi Yesu Asamala

[1]
Kodi Yesu asamalira
Nkasowa cimwemwe;
Ndikapsinjika ndi kuda nkhawa
M’njira yonse yaitari?

Chorus:
Ndidziwa amasamala, Inde ndikabvutika;
Ndithu masana ndi usiku amandisamalirane.

[2]
Kodi yesu asamalitsa
Mu’siku woopsa,
Pamene kwada zoopsa zadza,
Andisamalabe kodi?

[3]
Kodi Yesu asamalitsa
Ndikagwa m’mayeso?
Mwa za cisoni zosapumitsa,
Misozi usiku wonse?

[4]
Kodi Yesu asamalitsa
Poleka za dziko,
Ndiri kuthatha pafupi kufa
Kodi akundionadi?

Most Liked Songs
song image
1. Thanthwe Long’ambika

Khristu Mu Nyimbo

song image
2. Kodi Yesu Asamala

Khristu Mu Nyimbo

song image
3. Mukhale Ndine

Khristu Mu Nyimbo

song image
4. Bwinoli Tipita

Khristu Mu Nyimbo

song image
5. Sing’anga Mkuru Ndiye Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
6. Pokhala Mtendere

Khristu Mu Nyimbo

song image
7. Inenso

Khristu Mu Nyimbo

song image
8. Kuli Bwanji Kwathu

Khristu Mu Nyimbo

song image
9. Akulowa M’zipata

Khristu Mu Nyimbo

song image
10. Akristu Limbikani!

Khristu Mu Nyimbo

song image
11. Pakwitana Mbuye Wanga

Khristu Mu Nyimbo

song image
12. Ulemu Kwa Mulungu

Khristu Mu Nyimbo

song image
13. Inetu Ndifunadi

Khristu Mu Nyimbo

song image
14. Akristu Tiyeni

Khristu Mu Nyimbo

song image
15. Ambuyanga Yesu, Ndikonda Inu

Khristu Mu Nyimbo

song image
16. A M’dziko Akondweratu

Khristu Mu Nyimbo

song image
17. Dziko Ai, Koma Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
18. Akan’stogoza Ndinkako

Khristu Mu Nyimbo

song image
19. Pakakhala Cikondi

Khristu Mu Nyimbo

song image
20. Linda Usadandaule

Khristu Mu Nyimbo

song image
21. Bwenzi Lathu Ndiye Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
22. Ambuye, Ndiri Kudza

Khristu Mu Nyimbo

song image
23. Ndidze Pafupipa

Khristu Mu Nyimbo

song image
24. Tiribe Mzinda M’dzikoli

Khristu Mu Nyimbo

song image
25. Iripo Nyimbo Ndikonda

Khristu Mu Nyimbo

song image
26. Muli Dzuwa M’phiri Muja

Khristu Mu Nyimbo

song image
27. Mzimu Ndi Mtsogoziyo

Khristu Mu Nyimbo

song image
28. Poyemnda Ndi Mbuye

Khristu Mu Nyimbo

song image
29. Analonjeza Ambuye Wathu

Khristu Mu Nyimbo

song image
30. Ndidzamdziwa Mombolo Wanga

Khristu Mu Nyimbo