Ulemu Kwa Mulungu

[1]
Ulemu kwa Mlungu, Ambuye Wathu, Ankonda, napatsa ’fe Mwana wace;
Napatsatu moyo kuombola ’fe, Pa khomo la moyo natsegulatu.

Chorus:
Tamani Mbuyeyo, Dziko limvere ’Ye; Tamani Mbuyeyo, Anthu akondwetu;
Idzani kwa Tate mwa Mwana wace, Mpatseni ulemu anaconda ’fe.

[2]
Anapulumutsa mwazi wace Amene akhulupririra mwa ’Ye.
Ngakhale wocimwa koposa ndithu, Adzakhulukidwa mwa YEsuyo.

[3]
Anatiphunzitsa zopambanazo, Tikondwa mwa Yesu, Ambuye wathu;
Komabe ’dzaziwa kopambanadi, Pamene atenga ’fe, kumwambako.


Most Liked Songs
song image
1. Thanthwe Long’ambika

Khristu Mu Nyimbo

song image
2. Mukhale Ndine

Khristu Mu Nyimbo

song image
3. Kodi Yesu Asamala

Khristu Mu Nyimbo

song image
4. Bwinoli Tipita

Khristu Mu Nyimbo

song image
5. Sing’anga Mkuru Ndiye Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
6. Pokhala Mtendere

Khristu Mu Nyimbo

song image
7. Inenso

Khristu Mu Nyimbo

song image
8. Kuli Bwanji Kwathu

Khristu Mu Nyimbo

song image
9. Akulowa M’zipata

Khristu Mu Nyimbo

song image
10. Inetu Ndifunadi

Khristu Mu Nyimbo

song image
11. A M’dziko Akondweratu

Khristu Mu Nyimbo

song image
12. Akristu Tiyeni

Khristu Mu Nyimbo

song image
13. Ulemu Kwa Mulungu

Khristu Mu Nyimbo

song image
14. Akristu Limbikani!

Khristu Mu Nyimbo

song image
15. Pakwitana Mbuye Wanga

Khristu Mu Nyimbo

song image
16. Ndidze Pafupipa

Khristu Mu Nyimbo

song image
17. Ambuyanga Yesu, Ndikonda Inu

Khristu Mu Nyimbo

song image
18. Bwenzi Lathu Ndiye Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
19. Ambuye, Ndiri Kudza

Khristu Mu Nyimbo

song image
20. Muli Dzuwa M’phiri Muja

Khristu Mu Nyimbo

song image
21. Iripo Nyimbo Ndikonda

Khristu Mu Nyimbo

song image
22. Poyemnda Ndi Mbuye

Khristu Mu Nyimbo

song image
23. Akan’stogoza Ndinkako

Khristu Mu Nyimbo

song image
24. Dziko Ai, Koma Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
25. Tiribe Mzinda M’dzikoli

Khristu Mu Nyimbo

song image
26. Pakakhala Cikondi

Khristu Mu Nyimbo

song image
27. Linda Usadandaule

Khristu Mu Nyimbo

song image
28. Atate, Ndziperekatu

Khristu Mu Nyimbo

song image
29. Mtima Walemedwa Ko

Khristu Mu Nyimbo

song image
30. Ndidzamdziwa Mombolo Wanga

Khristu Mu Nyimbo