Muyamikeni Yesu

Language: Chichewa
Khristu Mu Nyimbo

Muyamikeni Yesu

[1]
Nyamikeni! Yesu wodala Mombolo!
Yimba cikondi cozizwitsadi!
Mkondwereni mkuru wa angelo m’Mwamba,
Dzina lace lilimekezedwe!
Monga mbusa asunga ana,
M’mikono mwace awanyamula.

Chorus:
Myamikeni! Ali wamkuru koposa;
Myamikeni m’nyimbo zokondwera.

[2]
Myamikeni! Yesu wodala Mombolo!
Zathu zocimwa nathira mwazi;
Ndiye Thanthwe lathu la cipulumutso,
Myamikeni Yesu wopacikikwa;
Mbukitseni! Yesu wotithangata,
Cikondi cosamariza ncace.

[3]
Myamikeni! Yesu wodala mombolo!
Khomo m’mwamba mumveka hosanna!
Yesu Mbuye alera nthawi zosatha;
Mbveke krona Wansembe ndi mfumu!
Kristu adza wogonjetsa dzikoli,
Mphavu ndi ulemu ndi za Yesu.


Most Liked Songs
song image
1. Thanthwe Long’ambika

Khristu Mu Nyimbo

song image
2. Mukhale Ndine

Khristu Mu Nyimbo

song image
3. Kodi Yesu Asamala

Khristu Mu Nyimbo

song image
4. Sing’anga Mkuru Ndiye Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
5. Bwinoli Tipita

Khristu Mu Nyimbo

song image
6. Pokhala Mtendere

Khristu Mu Nyimbo

song image
7. Inenso

Khristu Mu Nyimbo

song image
8. Kuli Bwanji Kwathu

Khristu Mu Nyimbo

song image
9. A M’dziko Akondweratu

Khristu Mu Nyimbo

song image
10. Akulowa M’zipata

Khristu Mu Nyimbo

song image
11. Inetu Ndifunadi

Khristu Mu Nyimbo

song image
12. Akristu Tiyeni

Khristu Mu Nyimbo

song image
13. Ulemu Kwa Mulungu

Khristu Mu Nyimbo

song image
14. Akristu Limbikani!

Khristu Mu Nyimbo

song image
15. Pakwitana Mbuye Wanga

Khristu Mu Nyimbo

song image
16. Dziko Ai, Koma Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
17. Ambuyanga Yesu, Ndikonda Inu

Khristu Mu Nyimbo

song image
18. Bwenzi Lathu Ndiye Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
19. Ambuye, Ndiri Kudza

Khristu Mu Nyimbo

song image
20. Muli Dzuwa M’phiri Muja

Khristu Mu Nyimbo

song image
21. Iripo Nyimbo Ndikonda

Khristu Mu Nyimbo

song image
22. Poyemnda Ndi Mbuye

Khristu Mu Nyimbo

song image
23. Akan’stogoza Ndinkako

Khristu Mu Nyimbo

song image
24. Ndidze Pafupipa

Khristu Mu Nyimbo

song image
25. Tiribe Mzinda M’dzikoli

Khristu Mu Nyimbo

song image
26. Pakakhala Cikondi

Khristu Mu Nyimbo

song image
27. Linda Usadandaule

Khristu Mu Nyimbo

song image
28. Mtima Walemedwa Ko

Khristu Mu Nyimbo

song image
29. Atate, Ndziperekatu

Khristu Mu Nyimbo

song image
30. Ali Kudza

Khristu Mu Nyimbo