Pa Mapazi Ace A Yesu

[1]
Pa mapazi ace Yesu, Ndimva mau acewo!
Ee, pafupi ndi Ambuye, N’khale nthawi zonsezo;
Pa mapazi ace Yesu, Ndiyang’anan m’mbuyomo,
Ee, cikondi cace conse, Cakopadi mtimanga.

[2]
Pa mapazi ace Yesu, Malo opambanawo;
Ndisiyepo chimo langa, Ndi kupeza mpumulo;
Pa mapazi ace Yesu, Ndimalira mtimanga,
Pomwe ndimapeza nsisi, Tsiku liri l onselo.

[3]
Inu yesu mdidalitse, Ndigwadira Inuyo;
Muyang’anetu pa ine, Nane ndikuoneni;
Ndikhaletu nawo Mtima, Monga Yesu Mbuyeyo,
Ndionetseretu yesu, Cilungamo cangaco.


Most Liked Songs
song image
1. Thanthwe Long’ambika

Khristu Mu Nyimbo

song image
2. Mukhale Ndine

Khristu Mu Nyimbo

song image
3. Kodi Yesu Asamala

Khristu Mu Nyimbo

song image
4. Sing’anga Mkuru Ndiye Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
5. Bwinoli Tipita

Khristu Mu Nyimbo

song image
6. Pokhala Mtendere

Khristu Mu Nyimbo

song image
7. Inenso

Khristu Mu Nyimbo

song image
8. Kuli Bwanji Kwathu

Khristu Mu Nyimbo

song image
9. A M’dziko Akondweratu

Khristu Mu Nyimbo

song image
10. Akulowa M’zipata

Khristu Mu Nyimbo

song image
11. Inetu Ndifunadi

Khristu Mu Nyimbo

song image
12. Akristu Tiyeni

Khristu Mu Nyimbo

song image
13. Ulemu Kwa Mulungu

Khristu Mu Nyimbo

song image
14. Akristu Limbikani!

Khristu Mu Nyimbo

song image
15. Pakwitana Mbuye Wanga

Khristu Mu Nyimbo

song image
16. Dziko Ai, Koma Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
17. Ambuyanga Yesu, Ndikonda Inu

Khristu Mu Nyimbo

song image
18. Bwenzi Lathu Ndiye Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
19. Ambuye, Ndiri Kudza

Khristu Mu Nyimbo

song image
20. Muli Dzuwa M’phiri Muja

Khristu Mu Nyimbo

song image
21. Iripo Nyimbo Ndikonda

Khristu Mu Nyimbo

song image
22. Poyemnda Ndi Mbuye

Khristu Mu Nyimbo

song image
23. Akan’stogoza Ndinkako

Khristu Mu Nyimbo

song image
24. Ndidze Pafupipa

Khristu Mu Nyimbo

song image
25. Tiribe Mzinda M’dzikoli

Khristu Mu Nyimbo

song image
26. Pakakhala Cikondi

Khristu Mu Nyimbo

song image
27. Linda Usadandaule

Khristu Mu Nyimbo

song image
28. Mtima Walemedwa Ko

Khristu Mu Nyimbo

song image
29. Atate, Ndziperekatu

Khristu Mu Nyimbo

song image
30. Ali Kudza

Khristu Mu Nyimbo