Lowetsa Yesu Mu Mtima

[1]
Kodi watopa nazo zoipa, Lowetsa Yesu mu Mtima;
Ngati ufuna kutembenuka, Lowetsa Yesu mu Mtima.

Chorus;
Leka kukayikatu; Usamkanenso lero,
Tsegula Mtima wako; Lowetsa Yesu mu Mtima.

[2]
Ukafuna kukhala woyera, Lowetsa Yesu mu Mtima;
Madzi osamba ali pafupi, Lowetsa Yesu mu Mtima.

[3]
Ngati muli bvuto mtimamo, Lowetsa Yesu mu Mtima;
Ngati wapereweza za m’dziko, Lowetsa Yesu mu Mtima.

[4]
Abwenzi akakusandukira, Lowetsa Yesu mu Mtima;
Ndiye bwenzi losatekeseka, Lowetsa Yesu mu Mtima.

[5]
Ngati uyimba nao odala, Lowetsa Yesu mu Mtima;
Udzalowe m’nyumba za mpumulo, Lowetsa Yesu mu Mtima.

Chorus (wotsiriza)
Leka kukayikaku; Usamkanenso lero,
Ndatsegula citseko, Kuti Yesu alowemo.

Most Liked Songs
song image
1. Thanthwe Long’ambika

Khristu Mu Nyimbo

song image
2. Kodi Yesu Asamala

Khristu Mu Nyimbo

song image
3. Mukhale Ndine

Khristu Mu Nyimbo

song image
4. Bwinoli Tipita

Khristu Mu Nyimbo

song image
5. Sing’anga Mkuru Ndiye Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
6. Pokhala Mtendere

Khristu Mu Nyimbo

song image
7. Akristu Limbikani!

Khristu Mu Nyimbo

song image
8. Inenso

Khristu Mu Nyimbo

song image
9. A M’dziko Akondweratu

Khristu Mu Nyimbo

song image
10. Kuli Bwanji Kwathu

Khristu Mu Nyimbo

song image
11. Akulowa M’zipata

Khristu Mu Nyimbo

song image
12. Ambuye, Ndiri Kudza

Khristu Mu Nyimbo

song image
13. Ali Kudza

Khristu Mu Nyimbo

song image
14. Ndidze Pafupipa

Khristu Mu Nyimbo

song image
15. Inetu Ndifunadi

Khristu Mu Nyimbo

song image
16. Muli Dzuwa M’phiri Muja

Khristu Mu Nyimbo

song image
17. Pakwitana Mbuye Wanga

Khristu Mu Nyimbo

song image
18. Akan’stogoza Ndinkako

Khristu Mu Nyimbo

song image
19. Akristu Tiyeni

Khristu Mu Nyimbo

song image
20. Bwenzi Lathu Ndiye Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
21. Ambuyanga Yesu, Ndikonda Inu

Khristu Mu Nyimbo

song image
22. Poyemnda Ndi Mbuye

Khristu Mu Nyimbo

song image
23. Yehova Ndi Mbusa Wangatu

Khristu Mu Nyimbo

song image
24. Dziko Ai, Koma Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
25. Bwera Wosocera! Bwera!

Khristu Mu Nyimbo

song image
26. Iripo Nyimbo Ndikonda

Khristu Mu Nyimbo

song image
27. Maso Ndi Maso

Khristu Mu Nyimbo

song image
28. Linda Usadandaule

Khristu Mu Nyimbo

song image
29. Kasupe Wa Madalitso

Khristu Mu Nyimbo

song image
30. Pakakhala Cikondi

Khristu Mu Nyimbo