Kodi Walemedwa M’mtima Mwako

[1]
Kodi walemedwa m’mtima mwako? Nena kwa Yesu, Nena kwa Yesu
Kodi uli kumva za cisoni? Nena kwa Yesu yekha.

CHORUS:
Nena kwa Yesu, nena kwa Yesu, Ndi bwenzi labwinotu.
Ndiye bwenzi lopambana onse, Nena kwa Yesu yekha.

[2]
Kodi ukulira mwa cisoni? Nena kwa yesu, nena kwa Yesu;
Kodi chimo lino labisika? Nena kwa yesu yekha.

[3]
Kodi umaopa za cisoni? Nena kwa Yesu, nena kwa Yesu;
Kodi ulikuda nkhawa m’mtima? Nena kwa Yesu yekha.

[4]
Kodi ukulingalira imfa? Nena kwa yesu, nena kwa Yesu;
Kodi ukulira kuti adze? Nena kwa Yesu yekha.


Most Liked Songs
song image
1. Thanthwe Long’ambika

Khristu Mu Nyimbo

song image
2. Mukhale Ndine

Khristu Mu Nyimbo

song image
3. Kodi Yesu Asamala

Khristu Mu Nyimbo

song image
4. Sing’anga Mkuru Ndiye Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
5. Bwinoli Tipita

Khristu Mu Nyimbo

song image
6. Pokhala Mtendere

Khristu Mu Nyimbo

song image
7. Inenso

Khristu Mu Nyimbo

song image
8. Kuli Bwanji Kwathu

Khristu Mu Nyimbo

song image
9. A M’dziko Akondweratu

Khristu Mu Nyimbo

song image
10. Akulowa M’zipata

Khristu Mu Nyimbo

song image
11. Inetu Ndifunadi

Khristu Mu Nyimbo

song image
12. Akristu Tiyeni

Khristu Mu Nyimbo

song image
13. Ulemu Kwa Mulungu

Khristu Mu Nyimbo

song image
14. Akristu Limbikani!

Khristu Mu Nyimbo

song image
15. Pakwitana Mbuye Wanga

Khristu Mu Nyimbo

song image
16. Dziko Ai, Koma Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
17. Ambuyanga Yesu, Ndikonda Inu

Khristu Mu Nyimbo

song image
18. Bwenzi Lathu Ndiye Yesu

Khristu Mu Nyimbo

song image
19. Ambuye, Ndiri Kudza

Khristu Mu Nyimbo

song image
20. Muli Dzuwa M’phiri Muja

Khristu Mu Nyimbo

song image
21. Iripo Nyimbo Ndikonda

Khristu Mu Nyimbo

song image
22. Poyemnda Ndi Mbuye

Khristu Mu Nyimbo

song image
23. Akan’stogoza Ndinkako

Khristu Mu Nyimbo

song image
24. Ndidze Pafupipa

Khristu Mu Nyimbo

song image
25. Tiribe Mzinda M’dzikoli

Khristu Mu Nyimbo

song image
26. Pakakhala Cikondi

Khristu Mu Nyimbo

song image
27. Linda Usadandaule

Khristu Mu Nyimbo

song image
28. Mtima Walemedwa Ko

Khristu Mu Nyimbo

song image
29. Atate, Ndziperekatu

Khristu Mu Nyimbo

song image
30. Ali Kudza

Khristu Mu Nyimbo